Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 34:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Anthu inu, talawani ndipo muona kuti Yehova ndi wabwino.+

      Wodala ndi munthu wamphamvu amene amathawira kwa iye.+

  • Salimo 125:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 125 Okhulupirira Yehova+

      Ali ngati phiri la Ziyoni,+ limene silingagwedezeke, koma lidzakhalapo mpaka kalekale.+

  • Salimo 146:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Wodala ndi munthu amene thandizo lake limachokera kwa Mulungu wa Yakobo,+

      Amene chiyembekezo chake chili mwa Yehova Mulungu wake,+

  • Miyambo 16:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Munthu wosonyeza kuzindikira pa zinthu adzapeza zabwino,+ ndipo wodala ndi munthu amene amakhulupirira Yehova.+

  • Yesaya 26:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Anthu amene ali ndi mtima wosagwedezeka mudzawateteza powapatsa mtendere wosatha,+ chifukwa amadalira inu.+

  • Yesaya 30:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Chotero Yehova azidzayembekezera kuti akukomereni mtima+ ndipo adzanyamuka kuti akuchitireni chifundo,+ pakuti Yehova ndi Mulungu amene amaweruza mwachilungamo.+ Odala+ ndi anthu onse amene amamuyembekezera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena