Genesis 41:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Kenako Farao anauza Yosefe kuti: “Popeza kuti Mulungu wakudziwitsa zonsezi,+ palibenso munthu wina wozindikira ndi wanzeru ngati iwe.+ Miyambo 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munthu wozindikira bwino, anthu amam’komera mtima.+ Koma njira ya anthu ochita zachinyengo imakhala yodzaza ndi zopweteka ndiponso mavuto.+
39 Kenako Farao anauza Yosefe kuti: “Popeza kuti Mulungu wakudziwitsa zonsezi,+ palibenso munthu wina wozindikira ndi wanzeru ngati iwe.+
15 Munthu wozindikira bwino, anthu amam’komera mtima.+ Koma njira ya anthu ochita zachinyengo imakhala yodzaza ndi zopweteka ndiponso mavuto.+