Salimo 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu munati: “Ndidzakupatsa nzeru ndi kukulangiza njira yoti uyendemo.+Ndidzakupatsa malangizo ndi kukuyang’anira.+ Miyambo 14:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mfumu imasangalala ndi wantchito wochita zinthu mozindikira,+ koma imakwiya ndi wantchito wochita zinthu zochititsa manyazi.+ 1 Akorinto 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Mulungu anasankha zopusa za dziko+ kuti achititse manyazi anthu anzeru, ndipo Mulungu anasankha zinthu zofooka za dziko kuti achititse manyazi+ zinthu zamphamvu.
8 Inu munati: “Ndidzakupatsa nzeru ndi kukulangiza njira yoti uyendemo.+Ndidzakupatsa malangizo ndi kukuyang’anira.+
35 Mfumu imasangalala ndi wantchito wochita zinthu mozindikira,+ koma imakwiya ndi wantchito wochita zinthu zochititsa manyazi.+
27 Koma Mulungu anasankha zopusa za dziko+ kuti achititse manyazi anthu anzeru, ndipo Mulungu anasankha zinthu zofooka za dziko kuti achititse manyazi+ zinthu zamphamvu.