Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 2:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Ndiyeno mfumuyo inapitiriza kuuza Simeyi kuti: “Iweyo wekha ukudziwa bwino mumtima mwako zoipa zonse zimene unachitira Davide bambo anga.+ Yehova akubwezera ndithu pamutu pako zoipa zimene unachita.+

  • Esitere 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno mfumu inanyamuka mokwiya+ kuchoka paphwando la vinyo ndi kupita kumunda wamaluwa wa panyumba ya mfumu. Pamenepo Hamani ananyamuka kuti apemphe Mfumukazi Esitere kuti ipulumutse moyo wake,+ chifukwa anaona kuti mfumu yatsimikiza zomupatsa chilango.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena