Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 16:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno Mfumu Davide inafika ku Bahurimu.+ Kumeneko inaona mwamuna wina wa m’banja la Sauli, dzina lake Simeyi,+ mwana wa Gera akutuluka ndipo anali kulankhula mawu onyoza.+

  • 2 Samueli 16:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pamenepo Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anapitiriza kuyenda mumsewu. Simeyi anali kuyenda m’mbali mwa phiri pafupi ndi Davide ndipo anali kuyenda akulankhula mawu onyoza.+ Iye analinso kuponya miyala akuyenda m’mbali mwa phirimo pafupi ndi Davide ndiponso anali kuwaza fumbi lambiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena