1 Samueli 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Yonatani anati: “N’zosatheka kuti iwe ukhale wolakwa! Koma ngati ndingadziwe zoipa zimene bambo anga akufuna kukuchitira, ukuganiza kuti sindingakuuze?”+ 1 Samueli 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho mudziwe zimenezi ndi kuona zimene mungachite, chifukwa atsimikiza kudzetsa tsoka+ pa mbuyanga ndi onse a m’nyumba yake, pakuti mbuye wathu ndi munthu wopanda pake,+ sitingathe kulankhula naye.” Salimo 112:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Woipa adzaona zimenezi ndipo adzasautsika.+ ש [Shin]Adzakukuta mano ndi kusungunuka.+ ת [Taw]Chikhumbo cha anthu oipa chidzatha.+ Miyambo 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mkwiyo wa mfumu uli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu,+ koma kukoma mtima kwake kuli ngati mame pazomera.+
9 Pamenepo Yonatani anati: “N’zosatheka kuti iwe ukhale wolakwa! Koma ngati ndingadziwe zoipa zimene bambo anga akufuna kukuchitira, ukuganiza kuti sindingakuuze?”+
17 Choncho mudziwe zimenezi ndi kuona zimene mungachite, chifukwa atsimikiza kudzetsa tsoka+ pa mbuyanga ndi onse a m’nyumba yake, pakuti mbuye wathu ndi munthu wopanda pake,+ sitingathe kulankhula naye.”
10 Woipa adzaona zimenezi ndipo adzasautsika.+ ש [Shin]Adzakukuta mano ndi kusungunuka.+ ת [Taw]Chikhumbo cha anthu oipa chidzatha.+
12 Mkwiyo wa mfumu uli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu,+ koma kukoma mtima kwake kuli ngati mame pazomera.+