Salimo 72:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzatsika ngati mvula pa udzu umene wadulidwa,+Ngati mvula yambiri yamvumbi imene imanyowetsa kwambiri nthaka.+ Hoseya 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndidzakhala ngati mame kwa Isiraeli,+ ndipo iye adzaphuka ngati maluwa okongola. Mizu yake idzazama ngati mtengo wa ku Lebanoni.
6 Adzatsika ngati mvula pa udzu umene wadulidwa,+Ngati mvula yambiri yamvumbi imene imanyowetsa kwambiri nthaka.+
5 Ine ndidzakhala ngati mame kwa Isiraeli,+ ndipo iye adzaphuka ngati maluwa okongola. Mizu yake idzazama ngati mtengo wa ku Lebanoni.