Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 23:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ulamuliro wake umakhala ngati kuwala kwa m’mawa pamene dzuwa lawala,+

      M’mawa wopanda mitambo.

      Umakhala ngati msipu womera padziko mvula ikakata, dzuwa n’kuwala.’+

  • Miyambo 16:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Nkhope ya mfumu ikawala, zimatanthauza moyo.+ Ndipo mafuno ake abwino ali ngati mtambo wa mvula yomalizira.+

  • Yesaya 58:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova azidzakutsogolerani+ nthawi zonse+ ndipo adzakukhutiritsani ngakhale m’dziko louma.+ Iye adzatsitsimula mafupa anu+ ndipo inu mudzakhala ngati munda wachinyontho chokwanira bwino,+ ndiponso ngati kasupe wamadzi yemwe madzi ake sanama.

  • Ezekieli 34:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Nkhosazo komanso malo ozungulira phiri langa ndidzawasandutsa dalitso.+ Ndidzagwetsa mvula yambiri pa nthawi yake. Kudzagwa mvula yambiri yamadalitso.+

  • Hoseya 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ife tidzamudziwa Yehova ndipo tidzayesetsa kuti timudziwe bwino.+ N’zosakayikitsa kuti iye adzafika ndithu ngati mmene m’bandakucha+ umafikira.+ Adzabwera kwa ife ngati mvula yambiri.+ Adzabwera ngati mvula yomalizira imene imanyowetsa kwambiri nthaka ya padziko lapansi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena