Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 29:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Iwo ankandidikirira ngati akudikira mvula,+

      Ndipo ankayasama kuti m’kamwa mwawo mugwere mvula yomalizira.+

  • Salimo 72:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Adzatsika ngati mvula pa udzu umene wadulidwa,+

      Ngati mvula yambiri yamvumbi imene imanyowetsa kwambiri nthaka.+

  • Miyambo 19:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mkwiyo wa mfumu uli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu,+ koma kukoma mtima kwake kuli ngati mame pazomera.+

  • Hoseya 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ife tidzamudziwa Yehova ndipo tidzayesetsa kuti timudziwe bwino.+ N’zosakayikitsa kuti iye adzafika ndithu ngati mmene m’bandakucha+ umafikira.+ Adzabwera kwa ife ngati mvula yambiri.+ Adzabwera ngati mvula yomalizira imene imanyowetsa kwambiri nthaka ya padziko lapansi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena