Yobu 29:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwo ankandidikirira ngati akudikira mvula,+Ndipo ankayasama kuti m’kamwa mwawo mugwere mvula yomalizira.+ Salimo 72:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzatsika ngati mvula pa udzu umene wadulidwa,+Ngati mvula yambiri yamvumbi imene imanyowetsa kwambiri nthaka.+
23 Iwo ankandidikirira ngati akudikira mvula,+Ndipo ankayasama kuti m’kamwa mwawo mugwere mvula yomalizira.+
6 Adzatsika ngati mvula pa udzu umene wadulidwa,+Ngati mvula yambiri yamvumbi imene imanyowetsa kwambiri nthaka.+