Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Esitere 7:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kenako mfumu inabwera kuchokera kumunda wamaluwa wa panyumba ya mfumu ndi kulowanso m’nyumba imene munali phwando la vinyo.+ Pamenepo inaona Hamani atadzigwetsa pampando wokhala ngati bedi+ pamene panali Esitere. Choncho mfumu inati: “Kodi ukufunanso kugwirira mfumukazi ine ndili m’nyumba mom’muno?” Mfumu italankhula,+ Hamani anamuphimba nkhope.

  • Miyambo 16:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mkwiyo wa mfumu umatanthauza amithenga a imfa,+ koma munthu wanzeru ndi amene amauziziritsa.+

  • Miyambo 20:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kuopsa kwa mfumu kuli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu.+ Aliyense woputa mkwiyo wake akuchimwira moyo wake womwe.+

  • Danieli 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mfumu itamva zimenezi inapsa mtima ndipo inakwiya kwambiri,+ moti inanena kuti amuna onse anzeru a m’Babulo ayenera kuphedwa.+

  • Mateyu 25:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 “Kenako adzauza a kumanzere kwake kuti, ‘Chokani pamaso panga+ inu otembereredwa. Pitani kumoto wosatha+ wokolezedwera Mdyerekezi ndi angelo ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena