Miyambo 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mkwiyo wa mfumu umatanthauza amithenga a imfa,+ koma munthu wanzeru ndi amene amauziziritsa.+