Mateyu 25:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Kenako adzauza amene ali kumanzere kwake kuti, ‘Chokani pamaso panga+ anthu otembereredwa inu. Pitani kumoto wosatha+ umene anakolezera Mdyerekezi ndi angelo ake.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:41 Nsanja ya Olonda,11/1/2008, ptsa. 5, 710/15/1995, tsa. 27 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 294-295
41 Kenako adzauza amene ali kumanzere kwake kuti, ‘Chokani pamaso panga+ anthu otembereredwa inu. Pitani kumoto wosatha+ umene anakolezera Mdyerekezi ndi angelo ake.+
25:41 Nsanja ya Olonda,11/1/2008, ptsa. 5, 710/15/1995, tsa. 27 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 294-295