Mateyu 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero ngati dzanja lako kapena phazi lako limakupunthwitsa, ulidule ndi kulitaya kutali.+ Ndi bwino kuti ukapeze moyo ulibe chiwalo chimodzi kapena uli wolumala kusiyana ndi kuti ukaponyedwe m’moto wosatha uli ndi manja onse awiri kapena mapazi onse awiri.+ Chivumbulutso 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mdyerekezi,+ amene anali kuwasocheretsa, adzaponyedwa m’nyanja yamoto ndi sulufule, mmene muli kale chilombo+ ndi mneneri wonyenga uja.+ Ndipo iwo adzazunzidwa usana ndi usiku kwamuyaya.
8 Chotero ngati dzanja lako kapena phazi lako limakupunthwitsa, ulidule ndi kulitaya kutali.+ Ndi bwino kuti ukapeze moyo ulibe chiwalo chimodzi kapena uli wolumala kusiyana ndi kuti ukaponyedwe m’moto wosatha uli ndi manja onse awiri kapena mapazi onse awiri.+
10 Mdyerekezi,+ amene anali kuwasocheretsa, adzaponyedwa m’nyanja yamoto ndi sulufule, mmene muli kale chilombo+ ndi mneneri wonyenga uja.+ Ndipo iwo adzazunzidwa usana ndi usiku kwamuyaya.