Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 5:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Tsopano ngati diso lako lakumanja limakuchimwitsa,* ulikolowole ndi kulitaya.+ Pakuti n’kwabwino kuti ukhale wopanda chiwalo chimodzi kusiyana n’kuti thupi lako lonse lidzaponyedwe+ m’Gehena.

  • Maliko 9:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 “Ndipo ngati dzanja lako limakuphunthwitsa, ulidule. Ndi bwino kuti ukapeze moyo ulibe chiwalo chimodzi, kusiyana n’kupita ku Gehena,* kumoto umene sungazimitsidwe, uli ndi manja onse awiri.+

  • Akolose 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho chititsani ziwalo za thupi+ lanu padziko lapansi kukhala zakufa+ ku dama, zinthu zodetsa, chilakolako cha kugonana,+ chikhumbo choipa, ndi kusirira kwa nsanje,+ kumene ndiko kulambira mafano.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena