9 Komanso ngati diso lako limakupunthwitsa ulikolowole n’kulitaya. Ndi bwino kuti ukapeze moyo uli ndi diso limodzi kusiyana ndi kuti ukaponyedwe mu Gehena* wamoto uli ndi maso onse awiri.+
47 Ngati diso lako limakuchimwitsa, ulitaye.+ Ndi bwino kuti ulowe mu ufumu wa Mulungu ndi diso limodzi, kusiyana n’kuponyedwa mu Gehena uli ndi maso onse awiri,+