Mateyu 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komanso ngati diso lako limakuchimwitsa* ulikolowole nʼkulitaya kutali. Ndi bwino kuti ukapeze moyo uli ndi diso limodzi kusiyana nʼkuti uponyedwe mu Gehena* wamoto uli ndi maso onse awiri.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:9 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,2/2018, tsa. 8 Yesu—Ndi Njira, tsa. 150 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, ptsa. 8-9
9 Komanso ngati diso lako limakuchimwitsa* ulikolowole nʼkulitaya kutali. Ndi bwino kuti ukapeze moyo uli ndi diso limodzi kusiyana nʼkuti uponyedwe mu Gehena* wamoto uli ndi maso onse awiri.+
18:9 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,2/2018, tsa. 8 Yesu—Ndi Njira, tsa. 150 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, ptsa. 8-9