Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 5:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Tsopano ngati diso lako lakumanja limakuchimwitsa,* ulikolowole ndi kulitaya.+ Pakuti n’kwabwino kuti ukhale wopanda chiwalo chimodzi kusiyana n’kuti thupi lako lonse lidzaponyedwe+ m’Gehena.

  • Mateyu 18:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Komanso ngati diso lako limakupunthwitsa ulikolowole n’kulitaya. Ndi bwino kuti ukapeze moyo uli ndi diso limodzi kusiyana ndi kuti ukaponyedwe mu Gehena* wamoto uli ndi maso onse awiri.+

  • Aroma 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pakuti ngati mukukhala motsatira zofuna za thupi, ndiye kuti mosakayikira mudzafa.+ Koma mukapha zochita za thupi+ mwa mzimu, mudzakhala ndi moyo.

  • Agalatiya 5:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndiponso anthu amene ali a Khristu Yesu, anapachika thupi lawo pamodzi ndi zikhumbo zake ndi zilakolako zake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena