1 Akorinto 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 koma ndikumenya thupi langa+ ndi kulitsogolera ngati kapolo, kuopera kuti, pambuyo poti ndalalikira kwa ena, ineyo ndingakhale wosayenera+ m’njira inayake. Agalatiya 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiponso anthu amene ali a Khristu Yesu, anapachika thupi lawo pamodzi ndi zikhumbo zake ndi zilakolako zake.+ Agalatiya 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti amene akufesa ndi cholinga chopindulitsa thupi lake, adzakolola chiwonongeko kuchokera m’thupi lakelo,+ koma amene akutsatira mzimu wa Mulungu+ adzakolola moyo wosatha kuchokera ku mzimuwo.+ Aefeso 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 kuti muvule umunthu wakale+ umene umagwirizana ndi khalidwe lanu lakale, umenenso ukuipitsidwa+ malinga ndi zilakolako zonyenga za umunthuwo.+ Akolose 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho chititsani ziwalo za thupi+ lanu padziko lapansi kukhala zakufa+ ku dama, zinthu zodetsa, chilakolako cha kugonana,+ chikhumbo choipa, ndi kusirira kwa nsanje,+ kumene ndiko kulambira mafano.
27 koma ndikumenya thupi langa+ ndi kulitsogolera ngati kapolo, kuopera kuti, pambuyo poti ndalalikira kwa ena, ineyo ndingakhale wosayenera+ m’njira inayake.
24 Ndiponso anthu amene ali a Khristu Yesu, anapachika thupi lawo pamodzi ndi zikhumbo zake ndi zilakolako zake.+
8 Pakuti amene akufesa ndi cholinga chopindulitsa thupi lake, adzakolola chiwonongeko kuchokera m’thupi lakelo,+ koma amene akutsatira mzimu wa Mulungu+ adzakolola moyo wosatha kuchokera ku mzimuwo.+
22 kuti muvule umunthu wakale+ umene umagwirizana ndi khalidwe lanu lakale, umenenso ukuipitsidwa+ malinga ndi zilakolako zonyenga za umunthuwo.+
5 Choncho chititsani ziwalo za thupi+ lanu padziko lapansi kukhala zakufa+ ku dama, zinthu zodetsa, chilakolako cha kugonana,+ chikhumbo choipa, ndi kusirira kwa nsanje,+ kumene ndiko kulambira mafano.