Yohane 6:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Mzimu ndi umene umapatsa moyo,+ mnofu n’ngopanda phindu. Mawu amene ndakuuzaniwa ndiwo mzimu+ ndiponso ndiwo moyo.+ Aroma 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti ngati mukukhala motsatira zofuna za thupi, ndiye kuti mosakayikira mudzafa.+ Koma mukapha zochita za thupi+ mwa mzimu, mudzakhala ndi moyo.
63 Mzimu ndi umene umapatsa moyo,+ mnofu n’ngopanda phindu. Mawu amene ndakuuzaniwa ndiwo mzimu+ ndiponso ndiwo moyo.+
13 Pakuti ngati mukukhala motsatira zofuna za thupi, ndiye kuti mosakayikira mudzafa.+ Koma mukapha zochita za thupi+ mwa mzimu, mudzakhala ndi moyo.