Agalatiya 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa amene akufesa nʼcholinga chopindulitsa thupi lake, adzakolola chiwonongeko kuchokera mʼthupi lakelo, koma amene akutsatira mzimu wa Mulungu adzakolola moyo wosatha kuchokera ku mzimuwo.+ Agalatiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:8 Nsanja ya Olonda,8/15/2008, tsa. 266/15/1995, tsa. 316/15/1988, ptsa. 19-20
8 Chifukwa amene akufesa nʼcholinga chopindulitsa thupi lake, adzakolola chiwonongeko kuchokera mʼthupi lakelo, koma amene akutsatira mzimu wa Mulungu adzakolola moyo wosatha kuchokera ku mzimuwo.+