Aroma 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti tikudziwa kuti umunthu wathu wakale unapachikidwa pamodzi ndi iye pamtengo,+ kuti thupi lathu lauchimo likhale ngati lakufa,+ kuti tisapitirize kukhala akapolo a uchimo.+ Akolose 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musamanamizane.+ Vulani umunthu+ wakale pamodzi ndi ntchito zake,
6 Pakuti tikudziwa kuti umunthu wathu wakale unapachikidwa pamodzi ndi iye pamtengo,+ kuti thupi lathu lauchimo likhale ngati lakufa,+ kuti tisapitirize kukhala akapolo a uchimo.+