Miyambo 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mkwiyo wa mfumu uli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu,+ koma kukoma mtima kwake kuli ngati mame pazomera.+ Mlaliki 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mzimu wa mtsogoleri ukakuukira, usachoke pamalo ako,+ chifukwa kudekha kumachepetsa machimo aakulu.+
12 Mkwiyo wa mfumu uli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu,+ koma kukoma mtima kwake kuli ngati mame pazomera.+
4 Mzimu wa mtsogoleri ukakuukira, usachoke pamalo ako,+ chifukwa kudekha kumachepetsa machimo aakulu.+