1 Mafumu 2:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pomaliza mfumu inatuma anthu kukaitana Simeyi,+ ndipo inamuuza kuti: “Udzimangire nyumba ku Yerusalemu ndipo uzikhala kumeneko. Usachoke kumeneko kupita kwina ndi kwina. Mlaliki 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Usafulumire kuchoka pamaso pake,+ ndipo usayambe kuchita zoipa.+ Pakuti mfumuyo idzachita zonse zimene ikufuna kuchita,+ Tito 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Asamanenere zoipa munthu aliyense, ndipo asakhale aukali.+ Koma akhale ololera,+ ndi ofatsa kwa anthu onse.+
36 Pomaliza mfumu inatuma anthu kukaitana Simeyi,+ ndipo inamuuza kuti: “Udzimangire nyumba ku Yerusalemu ndipo uzikhala kumeneko. Usachoke kumeneko kupita kwina ndi kwina.
3 Usafulumire kuchoka pamaso pake,+ ndipo usayambe kuchita zoipa.+ Pakuti mfumuyo idzachita zonse zimene ikufuna kuchita,+
2 Asamanenere zoipa munthu aliyense, ndipo asakhale aukali.+ Koma akhale ololera,+ ndi ofatsa kwa anthu onse.+