1 Mafumu 1:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Anthu onse oitanidwa amene anali ndi Adoniya anayamba kunjenjemera ndipo anaimirira, aliyense n’kumapita kwawo.+ Miyambo 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kuopsa kwa mfumu kuli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu.+ Aliyense woputa mkwiyo wake akuchimwira moyo wake womwe.+
49 Anthu onse oitanidwa amene anali ndi Adoniya anayamba kunjenjemera ndipo anaimirira, aliyense n’kumapita kwawo.+
2 Kuopsa kwa mfumu kuli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu.+ Aliyense woputa mkwiyo wake akuchimwira moyo wake womwe.+