Salimo 33:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kuti apulumutse moyo wawo ku imfa,+Ndi kuwasunga ndi moyo pa nthawi ya njala.+ Salimo 37:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawi yatsoka sadzachita manyazi,+Ndipo pa nthawi ya njala adzakhuta.+ Yesaya 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye ndi amene adzakhale pamalo apamwamba.+ Malo ake okhala adzakhala otetezeka m’matanthwe movuta kufikamo.+ Iye adzapatsidwa chakudya+ ndipo madzi ake sadzatha.”+ Hoseya 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndinakudziwa uli m’chipululu,+ m’dziko la matenda otenthetsa thupi.+
16 Iye ndi amene adzakhale pamalo apamwamba.+ Malo ake okhala adzakhala otetezeka m’matanthwe movuta kufikamo.+ Iye adzapatsidwa chakudya+ ndipo madzi ake sadzatha.”+