Salimo 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mikango yamphamvu ingakhale ndi chakudya chochepa ndipo ingamve njala.+Koma ofunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+ Salimo 37:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinali mwana, ndipo tsopano ndakula,+Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+ Salimo 111:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wapereka chakudya kwa anthu omuopa.+ י [Yohdh]Iye adzakumbukira pangano lake nthawi zonse.+ Luka 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma inu, pitirizani kufunafuna ufumu wake, ndipo zinthu zimenezi zidzawonjezedwa kwa inu.+
10 Mikango yamphamvu ingakhale ndi chakudya chochepa ndipo ingamve njala.+Koma ofunafuna Yehova sadzasowa chilichonse chabwino.+
25 Ndinali mwana, ndipo tsopano ndakula,+Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+