Nehemiya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo ndinati: “Inu Yehova Mulungu wakumwamba, ndinu Mulungu wamkulu ndi wochititsa mantha.+ Anthu amene amakukondani+ ndi kusunga malamulo anu+ mumawasungira pangano+ ndi kuwasonyeza kukoma mtima kosatha. Salimo 89:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Sindidzaphwanya pangano langa,+Ndipo sindidzasintha mawu otuluka pakamwa panga.+ Salimo 105:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wakumbukira pangano lake mpaka kalekale,+Wakumbukira lonjezo limene anapereka ku mibadwo 1,000,+
5 Pamenepo ndinati: “Inu Yehova Mulungu wakumwamba, ndinu Mulungu wamkulu ndi wochititsa mantha.+ Anthu amene amakukondani+ ndi kusunga malamulo anu+ mumawasungira pangano+ ndi kuwasonyeza kukoma mtima kosatha.