Deuteronomo 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye.+ Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa,+ amene sakondera+ munthu aliyense ndipo salandira chiphuphu.+ Salimo 47:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti Yehova, Wam’mwambamwamba, ndi wochititsa mantha,+Ndiye Mfumu yaikulu padziko lonse lapansi.+ Danieli 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo ndinayamba kupemphera kwa Yehova Mulungu wanga ndi kuvomereza machimo athu kuti:+ “Inu Yehova Mulungu woona, Mulungu wamkulu+ ndi wochititsa mantha. Anthu amene amakukondani ndi kusunga malamulo anu+ mumawasungira pangano+ ndi kuwasonyeza kukoma mtima kosatha.+
17 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye.+ Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa,+ amene sakondera+ munthu aliyense ndipo salandira chiphuphu.+
2 Pakuti Yehova, Wam’mwambamwamba, ndi wochititsa mantha,+Ndiye Mfumu yaikulu padziko lonse lapansi.+
4 Pamenepo ndinayamba kupemphera kwa Yehova Mulungu wanga ndi kuvomereza machimo athu kuti:+ “Inu Yehova Mulungu woona, Mulungu wamkulu+ ndi wochititsa mantha. Anthu amene amakukondani ndi kusunga malamulo anu+ mumawasungira pangano+ ndi kuwasonyeza kukoma mtima kosatha.+