Deuteronomo 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye. Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa, amene sakondera munthu aliyense+ ndipo salandira chiphuphu. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:17 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Yandikirani, tsa. 114
17 Chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye. Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa, amene sakondera munthu aliyense+ ndipo salandira chiphuphu.