Deuteronomo 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye.+ Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa,+ amene sakondera+ munthu aliyense ndipo salandira chiphuphu.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:17 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Yandikirani, tsa. 114
17 Pakuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye.+ Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa,+ amene sakondera+ munthu aliyense ndipo salandira chiphuphu.+