Machitidwe 10:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Petulo atamva zimenezi, anayamba kulankhula kuti: “Ndazindikira ndithu kuti Mulungu alibe tsankho.+ Aroma 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa Mulungu alibe tsankho.+
34 Petulo atamva zimenezi, anayamba kulankhula kuti: “Ndazindikira ndithu kuti Mulungu alibe tsankho.+