Deuteronomo 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye. Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa, amene sakondera munthu aliyense+ ndipo salandira chiphuphu. 2 Mbiri 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Muziopa Yehova+ ndipo muzisamala pochita zinthu, chifukwa Yehova Mulungu wathu si wopanda chilungamo+ kapena watsankho,+ ndipo salandira chiphuphu.”+ Machitidwe 10:34, 35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Petulo atamva zimenezi, anayamba kulankhula kuti: “Ndazindikira ndithu kuti Mulungu alibe tsankho.+ 35 Iye amalandira munthu wochokera mu mtundu uliwonse, amene amamuopa ndi kuchita chilungamo.+
17 Chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye. Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa, amene sakondera munthu aliyense+ ndipo salandira chiphuphu.
7 Muziopa Yehova+ ndipo muzisamala pochita zinthu, chifukwa Yehova Mulungu wathu si wopanda chilungamo+ kapena watsankho,+ ndipo salandira chiphuphu.”+
34 Petulo atamva zimenezi, anayamba kulankhula kuti: “Ndazindikira ndithu kuti Mulungu alibe tsankho.+ 35 Iye amalandira munthu wochokera mu mtundu uliwonse, amene amamuopa ndi kuchita chilungamo.+