Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 18:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano ndadziwa kuti Yehova ndi wamkulu kuposa milungu ina yonse,+ chifukwa cha zimene anachitira anthu amene ankachita zinthu modzikuza pamaso pa anthu ake.”

  • 2 Mbiri 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Nyumba imene ndikumangayi idzakhala yochititsa chidwi, chifukwa Mulungu wathu ndi wamkulu kuposa milungu ina yonse.

  • Salimo 97:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Chifukwa inu Yehova, ndinu Wamʼmwambamwamba woyenera kulamulira dziko lonse lapansi.

      Ndinu wokwezeka kwambiri kuposa milungu ina yonse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena