Deuteronomo 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye. Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa, amene sakondera munthu aliyense+ ndipo salandira chiphuphu. 2 Mbiri 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Muziopa Yehova+ ndipo muzisamala pochita zinthu, chifukwa Yehova Mulungu wathu si wopanda chilungamo+ kapena watsankho,+ ndipo salandira chiphuphu.”+ Aroma 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa Mulungu alibe tsankho.+
17 Chifukwa Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wa milungu+ ndi Mbuye wa ambuye. Iye ndi Mulungu wamkulu, wamphamvu ndi woopsa, amene sakondera munthu aliyense+ ndipo salandira chiphuphu.
7 Muziopa Yehova+ ndipo muzisamala pochita zinthu, chifukwa Yehova Mulungu wathu si wopanda chilungamo+ kapena watsankho,+ ndipo salandira chiphuphu.”+