Aroma 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Paja anthu ongomva Chilamulo, Mulungu samawaona kuti ndi olungama koma amene amatsatira Chilamulo ndi amene adzaonedwe kuti ndi olungama.+ 1 Akorinto 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tonsefe tinabatizidwa ndi mzimu umodzi kuti tikhale thupi limodzi. Kaya ndife Ayuda kapena Agiriki, akapolo kapena anthu aufulu, tonsefe tinalandira* mzimu umodzi. Agalatiya 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Palibe Myuda kapena Mgiriki,+ palibe kapolo kapena mfulu,+ palibenso mwamuna kapena mkazi+ chifukwa nonsenu ndinu amodzi mwa Khristu Yesu.+
13 Paja anthu ongomva Chilamulo, Mulungu samawaona kuti ndi olungama koma amene amatsatira Chilamulo ndi amene adzaonedwe kuti ndi olungama.+
13 Tonsefe tinabatizidwa ndi mzimu umodzi kuti tikhale thupi limodzi. Kaya ndife Ayuda kapena Agiriki, akapolo kapena anthu aufulu, tonsefe tinalandira* mzimu umodzi.
28 Palibe Myuda kapena Mgiriki,+ palibe kapolo kapena mfulu,+ palibenso mwamuna kapena mkazi+ chifukwa nonsenu ndinu amodzi mwa Khristu Yesu.+