Deuteronomo 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa mawu a chilamulowo ali pafupi kwambiri ndi inu, ali mʼkamwa mwanu ndi mumtima mwanu+ kuti muwatsatire.+ Ezekieli 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako ndinawapatsa malamulo anga ndi kuwadziwitsa zigamulo zanga+ kuti munthu amene akuzitsatira akhale ndi moyo.+ Yakobo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komabe muzichita zimene mawu amanena,+ osati kungomva chabe, nʼkumadzipusitsa ndi maganizo abodza.
14 Chifukwa mawu a chilamulowo ali pafupi kwambiri ndi inu, ali mʼkamwa mwanu ndi mumtima mwanu+ kuti muwatsatire.+
11 Kenako ndinawapatsa malamulo anga ndi kuwadziwitsa zigamulo zanga+ kuti munthu amene akuzitsatira akhale ndi moyo.+
22 Komabe muzichita zimene mawu amanena,+ osati kungomva chabe, nʼkumadzipusitsa ndi maganizo abodza.