Salimo 105:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amakumbukira pangano lake mpaka kalekale,+Lonjezo limene anapereka* ku mibadwo 1,000.+