Deuteronomo 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu mukudziwa bwino kuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu woona, Mulungu wokhulupirika, amene amasunga pangano lake ndiponso amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa anthu amene amamukonda ndi kusunga malamulo ake ku mibadwo 1,000.+ Luka 1:72, 73 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 72 Adzakwaniritsa zimene analonjeza makolo athu akale ndipo adzawasonyeza chifundo. Iye adzakumbukira pangano lake loyera,+ 73 lumbiro limene analumbira kwa kholo lathu Abulahamu,+
9 Inu mukudziwa bwino kuti Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu woona, Mulungu wokhulupirika, amene amasunga pangano lake ndiponso amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa anthu amene amamukonda ndi kusunga malamulo ake ku mibadwo 1,000.+
72 Adzakwaniritsa zimene analonjeza makolo athu akale ndipo adzawasonyeza chifundo. Iye adzakumbukira pangano lake loyera,+ 73 lumbiro limene analumbira kwa kholo lathu Abulahamu,+