Yobu 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Elihu mwana wa Barakeli mbadwa ya Buza anati:“Ine ndine wamng’onoNdipo amuna inu ndinu achikulire.+N’chifukwa chake ndinabweza mawu anga ndipo ndinaopaKukuuzani zimene ndikudziwa. Salimo 71:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngakhale nditakalamba ndi kumera imvi, inu Mulungu musandisiye,+Kufikira nditanena za dzanja lanu lamphamvu ku m’badwo wotsatira,+Kufikira nditanena za mphamvu zanu kwa onse obwera m’tsogolo.+
6 Kenako Elihu mwana wa Barakeli mbadwa ya Buza anati:“Ine ndine wamng’onoNdipo amuna inu ndinu achikulire.+N’chifukwa chake ndinabweza mawu anga ndipo ndinaopaKukuuzani zimene ndikudziwa.
18 Ngakhale nditakalamba ndi kumera imvi, inu Mulungu musandisiye,+Kufikira nditanena za dzanja lanu lamphamvu ku m’badwo wotsatira,+Kufikira nditanena za mphamvu zanu kwa onse obwera m’tsogolo.+