1 Samueli 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 (Eli anali ndi zaka 98, ndipo maso ake anangokhala tong’o koma sanali kuona.)+ Salimo 37:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinali mwana, ndipo tsopano ndakula,+Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+ Salimo 71:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musanditaye nthawi ya ukalamba wanga.+Musandisiye pa nthawi imene mphamvu zanga zikutha.+
25 Ndinali mwana, ndipo tsopano ndakula,+Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+