Salimo 78:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mbadwa zawo sitikuzibisira mawu ophiphiritsawa,+Ndipo tidzawasimba ngakhale ku mibadwo ya m’tsogolo.+Tidzasimba ntchito zotamandika za Yehova ndi mphamvu zake,+Komanso zinthu zodabwitsa zimene wachita.+
4 Mbadwa zawo sitikuzibisira mawu ophiphiritsawa,+Ndipo tidzawasimba ngakhale ku mibadwo ya m’tsogolo.+Tidzasimba ntchito zotamandika za Yehova ndi mphamvu zake,+Komanso zinthu zodabwitsa zimene wachita.+