Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Koma khalani tcheru ndipo musamale moyo wanu,+ kuti musaiwale zinthu zimene maso anu anaona,+ ndi kuti mitima yanu isaiwale zinthu zimenezo masiku onse a moyo wanu.+ Ana anu ndi zidzukulu zanu muziwauza za zinthu zimenezo,+

  • Deuteronomo 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 ndi kuwakhomereza mwa ana ako.+ Uzilankhula nawo za mawuwo ukakhala pansi m’nyumba mwako, poyenda pamsewu, pogona+ ndi podzuka.

  • Deuteronomo 6:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pamenepo mwana wakoyo udzamuyankhe kuti, ‘Tinakhala akapolo a Farao ku Iguputo, koma Yehova anatitulutsa ku Iguputoko ndi dzanja lamphamvu.+

  • Salimo 145:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Anthu adzatamanda ntchito zanu ku mibadwomibadwo,+

      Ndipo adzasimba za zochita zanu zamphamvu.+

  • Yoweli 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Fotokozerani ana anu za zinthu zimenezi. Ana anu adzafotokozere ana awo, ndipo ana a ana anuwo adzafotokozerenso m’badwo wotsatira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena