Miyambo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwana wanga, usaiwale lamulo langa,+ ndipo mtima wako usunge malamulo anga.+ Miyambo 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mwana wanga, sunga mawu anga+ ndipo usunge malamulo anga ngati chuma chamtengo wapatali.+ Aheberi 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiye chifukwa chake n’kofunika kuti tiganizire mozama, kuposa nthawi zonse, zinthu zimene tinamva,+ kuti tisatengeke pang’onopang’ono n’kusiya chikhulupiriro.+
2 Ndiye chifukwa chake n’kofunika kuti tiganizire mozama, kuposa nthawi zonse, zinthu zimene tinamva,+ kuti tisatengeke pang’onopang’ono n’kusiya chikhulupiriro.+