Salimo 73:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma ine phazi langa linangotsala pang’ono kupatuka,+Mapazi anga anangotsala pang’ono kuterereka.+ Aheberi 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chenjerani abale, kuti pakati panu, wina asachoke kwa Mulungu wamoyo n’kukhala ndi mtima woipa wopanda chikhulupiriro.+ 2 Petulo 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho inu okondedwa, popeza mukudziwiratu zimenezi,+ chenjerani kuti musasochere pokopeka ndi zolakwa za anthu ophwanya malamulowo, kuopera kuti mungalephere kukhala olimba ndipo mungagwe.+ Chivumbulutso 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe, ndakupeza ndi mlandu wakuti wasiya chikondi chimene unali nacho poyamba.+
12 Chenjerani abale, kuti pakati panu, wina asachoke kwa Mulungu wamoyo n’kukhala ndi mtima woipa wopanda chikhulupiriro.+
17 Choncho inu okondedwa, popeza mukudziwiratu zimenezi,+ chenjerani kuti musasochere pokopeka ndi zolakwa za anthu ophwanya malamulowo, kuopera kuti mungalephere kukhala olimba ndipo mungagwe.+