Salimo 38:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ine ndinati: “Ngati simundiyankha adani anga adzasangalala chifukwa cha kusautsika kwanga.+Phazi langa likaterereka,+ iwo adzadzikweza pamaso panga.”+ Salimo 94:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene ndinanena kuti: “Phazi langa literereka,”+Kukoma mtima kwanu kosatha, inu Yehova, kunandichirikiza.+
16 Ine ndinati: “Ngati simundiyankha adani anga adzasangalala chifukwa cha kusautsika kwanga.+Phazi langa likaterereka,+ iwo adzadzikweza pamaso panga.”+
18 Pamene ndinanena kuti: “Phazi langa literereka,”+Kukoma mtima kwanu kosatha, inu Yehova, kunandichirikiza.+