1 Samueli 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+ Salimo 37:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ngakhale atapunthwa, sadzagweratu,+Pakuti Yehova wamugwira dzanja.+ Salimo 117:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene watisonyeza ndi kwakukulu.+Ndipo choonadi+ cha Yehova chidzakhalapobe mpaka kalekale.Tamandani Ya, anthu inu!+ Maliro 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+
9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+
2 Pakuti kukoma mtima kosatha kumene watisonyeza ndi kwakukulu.+Ndipo choonadi+ cha Yehova chidzakhalapobe mpaka kalekale.Tamandani Ya, anthu inu!+
22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+