Salimo 94:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene ndinanena kuti: “Phazi langa literereka,”+Kukoma mtima kwanu kosatha, inu Yehova, kunandichirikiza.+ Salimo 100:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti Yehova ndi wabwino.+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapo mpaka kalekale,+Ndipo kukhulupirika kwake kudzakhalapo ku mibadwomibadwo.+ Maliro 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+
18 Pamene ndinanena kuti: “Phazi langa literereka,”+Kukoma mtima kwanu kosatha, inu Yehova, kunandichirikiza.+
5 Pakuti Yehova ndi wabwino.+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapo mpaka kalekale,+Ndipo kukhulupirika kwake kudzakhalapo ku mibadwomibadwo.+
22 Chifukwa cha kukoma mtima kosatha+ kwa Yehova, ife sitinafafanizidwe,+ ndipo chifundo chake sichidzatha.+