Salimo 38:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ine ndinati: “Ngati simundiyankha adani anga adzasangalala chifukwa cha kusautsika kwanga.+Phazi langa likaterereka,+ iwo adzadzikweza pamaso panga.”+ Salimo 121:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye sangalole kuti phazi lako lipunthwe.+Amene amakuyang’anira sangawodzere.+
16 Ine ndinati: “Ngati simundiyankha adani anga adzasangalala chifukwa cha kusautsika kwanga.+Phazi langa likaterereka,+ iwo adzadzikweza pamaso panga.”+