Salimo 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chitani zimenezi kuti mdani wanga asanene kuti: “Ndamugonjetsa!”Kutinso adani anga asakondwere chifukwa chakuti ine ndadzandira.+ Salimo 35:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Inu Yehova Mulungu wanga, mundiweruze mogwirizana ndi chilungamo chanu,+Musalole kuti adani anga akondwere ndi kusautsika kwanga.+
4 Chitani zimenezi kuti mdani wanga asanene kuti: “Ndamugonjetsa!”Kutinso adani anga asakondwere chifukwa chakuti ine ndadzandira.+
24 Inu Yehova Mulungu wanga, mundiweruze mogwirizana ndi chilungamo chanu,+Musalole kuti adani anga akondwere ndi kusautsika kwanga.+